Yesu Nyali Ya Dziko
[1]
Ha! Nayimba angelo, Yesu nyali ya dziko;
Mwana wabadwa Mfumu, Yesu nyali ya dziko.
Chorus:
Yenda m’kuunika kwabwiniko,
Idza kumene kuli cifuno,
Kuwala kwa msana ndi usiku;
Yesu, nyali ya dziko.
[2]
Mapfukonu kondwani, Yesu nyali ya dziko;
Kondwani ndi a m’mwamba, Yesu nyali ya dziko.
[3]
M’mwamba amlekeza, Yesu nyali ya dziko;
Yesu Mbuye wosatha, Yesu nyali ya dziko.
[4]
Mfumu ya mtenderedi, Yesu nyali ya dziko;
Dzuwa la cilungamo, Yesu nyali ya dziko.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.