Loading Songs...

Mukhale Ndine

[1]
Mukhale ndine dzuwa lalowa, Wagwa utsiku bwenzi lisowa, Ndiribe wina wondithandiza, Wa mphamvu ndinu, mukhale ndinetu.

[2]
Kamoyo kanga katha leroli, Zidzacokanso zinthu za dziko,
Zimasinthika zoonekazo, Simusinthika mkhale ndinetu.

[3]
Koma kale mnakhalitsa pano, Mukhale ndine musacokenso,
Simpempha kuti Mbuye mutsotse, Komatu mukhalitse ndinetu.

[4]
Ndifuna inu tsiku lonselo, Ndi mphamvu yanu ndidzasungika,
Mokatsogola sindiopai, Msana, usiku mkhale ndinetu.

[5]
Adani sindiopa mulipo, Muletse tsoka ndi cisonici,
Ikadza imfa ndzalima mtima, M’imfa ndi moyo mkhale ndinetu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

18 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

ABIDE WITH ME ABIDE WITH ME
Hymns Of Comfort
Glory Glory
Songs On Request
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort