Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Kodi Yesu Asamala

[1]
Kodi Yesu asamalira
Nkasowa cimwemwe;
Ndikapsinjika ndi kuda nkhawa
M’njira yonse yaitari?

Chorus:
Ndidziwa amasamala, Inde ndikabvutika;
Ndithu masana ndi usiku amandisamalirane.

[2]
Kodi yesu asamalitsa
Mu’siku woopsa,
Pamene kwada zoopsa zadza,
Andisamalabe kodi?

[3]
Kodi Yesu asamalitsa
Ndikagwa m’mayeso?
Mwa za cisoni zosapumitsa,
Misozi usiku wonse?

[4]
Kodi Yesu asamalitsa
Poleka za dziko,
Ndiri kuthatha pafupi kufa
Kodi akundionadi?


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Ancient Words Ancient Words Golden Bells
HOW GREAT THOU ART HOW GREAT THOU ART Songs Of Prayer And Praise
A Wonderful Savior A Wonderful Savior Christ In Song Hymnal
He Hideth My Soul He Hideth My Soul Golden Bells