Bwinoli Tipita
[1]
Kuli dziko labwino m’mwamba
Lakuwala Koposa dzuwa,
Ndi Atate akonza malo,
Pokhalira ife komweko.
CHORUS:
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
[2]
Tidzayimba komeko nyimbo,
Za abwino omwera Yesu,
Sitizamvatu zisonizo
Tidzakondwa masiku onse.
[3]
Tidzatama Atate wathu,
Kuti iye ‘napatsa Yesu
Kuchotsera zocimwa zones,
Ndikutidalitsira ife.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.