Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Yesu Mundilankhule

[1]
Yesu, Mundilankhule, Mau ofatsawo;
Mndinong’oneze kuti, SUlitu wekha ’we.
Mtima munditsegule, Kuti ndimvere ’Nu;
Mdzaze mu Mtima wanga, Kuti ndikondwedi.

Chorus:
Mundinong’onezetu, mwa nsisi zanuzo
Udzagonjetsa ndithu, Udzamasukadi.
Mundilankhule, Mbuye, Tsiku ndi tsikunso,
Ndimvetu mau anu, Sulita wekha ’we

[2]
Yesu, munene mau Ndi ana anuwo,
Kuyang’anira Inu, Muwapjunzitsetu;
Kuti apereketu Moyo kwa inuyo,
Udze ufumu wanu, Kuti ’dzaone ’Nu.

[3]
Kale munaonetsa Kufuna kwanuko,
Yanga ndidziwe ntchito, Ndicite zanuzo;
Ndilemekeze Inu, Kwa anthu onsewo,
Ncite kufuna kwanu, Masiku onsewo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal