Loading Songs...

Yesu Anditsogozatu

[1]
Yesu anditsogozatu; Nanganso ndifunanji?
Kodi ndimkaika Iye, Wonditsogolerayo?
Mtenderewo andipatsa, Mwa cikhulupiroco!
Mkana lindigwere bvuto, Yesu athangata ’ne’
Mkana lindigwere bvuto, Yesu athangata ’ne;

[2]
Yesu anditsogolera, Andisangalatsanso;
Athandiza ’ne m’mayeso, Andidyetsa mkatewo;
Nkana ndiri wakutopa, Ludzu landigwiranso,
Mu Thanthwelo Yesu Kristu, Ndionamo madziwo;
Mu Thanthwelo Yesu Kristu, Ndionamo madziwo;

[3]
Yesu anditsogolera, Mwa cikondi caceco!
Alonjeza ’ne mpumulo, Mnyumba ya Atateyo;
Nkadzauka tsiku lijaa, Ndidzapita mmwambamo,
Ndidzayimba kosaleka, Yesu natsogoza ’ne;
Ndidzayilmba kosaleka, Yesu natsogoza ’ne;



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise
GIVE THANKS GIVE THANKS
Songs Of Prayer And Praise