Yesu Andisungetu!
[1]
Yesu andisungetu! Ndi mphamvu yaceyo;
Dziko lisandidetse; Kuti nditsate ’Ye.
Chorus:
Yesu andisungetu! Mbuye ndipempha ’Nu;
Inetu ndine cabe, cabe, Inu ndi zonsezo.
[2]
Yesu andisungetu! Nditumikire ’Ye;
Ndicitetu kufuna, Kwa Yesu, Mbuyeyo.
[3]
Yesu andisungetu! Dziko ndilisiya;
Ndikhaletu wofatsa, Woyera mtimamo.
[4]
Yesu andisungetu! N’khaletu waceyo;
N’khaletu wace yekha, Ku nthawi zonsezo.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.