Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Yemwe Afuna

[1]
Yemwe alikumwa! Pfula mau:
Tumizani mthenga m’dziko monsemo;
Lalikani anthu kuli konseko;
Yemwe afuna adze.

CHORUS:
Omwe afuna, omwe afuna
Uza za chimwemwe m’dambo ndi m’phiri;
Atate wokonda aitana’ce
Omwe afuna adze.

[2]
Yemwe alikudza, asachedwe,
Pakhomo patseguka, lowa msanga;
Yesu ndiye njiratu yakuona
Yemwe afuna adze

[3]
Yemwe afunitsa za mtendere,
Yemwe afunitsa adzakhalabe;
Yemwe afunitsa moyo wosatha:
Yemwe afuna adze.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal