Loading Songs...

Yehova Ndi Mbusa Wangatu

[1]
Yehova ndi Mbusa, Sin’dzasowai, Ndigona ku busa La msipu wace
Anditsogolera Ku madzi ace, Anditsitsimutsa Ndi mphamvu yace.

[2]
Anditsogolera M’mabande mwace, Cifukwa ca dzina Lokondwedwalo.
Ngakhale ndiyenda pafupi infa, H! sindiopa Zoipa zonse.

[3]
Cibonga ndi ndodo Za Mbusa wanga Zindisangalatsa Masiku onse.
Mundiyalikira Pa maso panga, Mkkuona kwa mdani Cakudya canga.

[4]
Mudzoza mafuta Pa mutu panga, Mwadzaza cifundo Mu cikho canga
Udzanditsatira Ukoma wanu, Ndidzakhala nanu masiku onse.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

I WILL CALL UPON THE LORD I WILL CALL UPON THE LORD
Songs Of Prayer And Praise
Immortally Arrayed Immortally Arrayed
Songs On Request
Listen To Our Hearts Listen To Our Hearts
Songs On Request
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Hymns Of Comfort
He Hideth My Soul He Hideth My Soul
Golden Bells
Kaa Nami Kaa Nami
Kiswahili Praise And Worship