Loading Songs...

Wakukonzeka Pakubwera Mkwati

[1]
Wakonzeka pakubweraa mkwatiyo, Mkwatiyo?
Wakonzeka pakubwera mkwatiyo, mkwatiyo?
Onani adza; onani adza; Konzeka akubwera mkwatiyo.

CHORUS:
Onani Mkwati, Yesu abweratu! Onani mkwati, Yesu abweratu!
Yang’anadza, yang’ana adza! Konzeka akubwera mkwatiyo.

[2]
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Akudza msanga; akudza msanga; konzeka moyo wanga wonse ’we

[3]
Tidzakomana naye, Mkwatiyo, Mkwatiyo!
Tidzakomana naye, Mkwatiyo, Mkawtiyo!
Adzadi Yesu; adzadi Yesu; Tidzakomana naye Mkwatiyo

[4]
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, Kwa ’Ye
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, Kwa ’Ye
Yang’ana adza; yang’ana adza; Yimbani, Aleluya, adzatu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Servant’s Song Servant’s Song
Songs On Request
Victory In Jesus Victory In Jesus
Golden Bells
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Hymns Of Comfort
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs
What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal
Abide With Me Abide With Me
Golden Bells