Loading Songs...

Uzeni Nthano Yakale

[1]
Uze nthano yakale, Ya za kumwambako,
Za Yesu wacifundo, Za Yesu wokonda;
Pang’ono pang’onotu, monga kwa kamwana,
Poti ndiri wotopa, wopanda thandizo.

Chorus:
Nthano yakale uze, Nthano yakale uze,
Nthano yakale uze, Ya Yesu wokonda.

[2]
Pang’ono ndi pang’ono, Motsimikizadi;
Pakuti ndaipadi, Yesu nandifera;
Nthano yonseyo uze, Musacite mphwayi,
M’nthawi yonse ya bvuto, Andisangalatsa.

[3]
Nenatu yomwe ija, Ukhala ndi mantha,
Kuti dziko loipa, Ndilikondetsetsa;
Ulemu wa dzikowu Uyamba m’moyomu,
Uze nthano yakale; Yesu akuciza.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request
Joy To The World Joy To The World
Caroling Songs
Listen To Our Hearts Listen To Our Hearts
Songs On Request
Amazing Grace Amazing Grace
Spiritual Songs
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise
Blessed Assurance Blessed Assurance
Spiritual Songs