Loading Songs...

Ugoneranji Mwana Wa Mfumu

[1]
Ugoneranji mwana wa mfumu
Kwinanso wayandikira mmwamba?
Dzuka, nyamuka, ubvale za nkhondo;
Bweratu nthawi isanathei.

[2]
Anthu a mdziko adzanjenjemera,
Adzaopsedwa ndi kudza kwace;
Mvetsa migugu abwera Ambuye,
Mwana wa mfumu usacedwatu.

[3]
Usacedwenso ndi zinthu za mdziko
Ulemerero udzathadi phe!
Dula zinsinga zolimba za mdani,
Mwana wa mfumu kondwera ndithu.

[4]
Usayang’anetu kwina iyai,
Ona nonse kuwala m’mapiri monsemo,
Mwana wa mfumu zileke zonse.
Yembekeza ufumu wace;



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

He Hideth My Soul He Hideth My Soul
Golden Bells
Hide Me, Rock Of Ages Hide Me, Rock Of Ages
Songs On Request
What A Friend What A Friend
Golden Bells
I WILL CALL UPON THE LORD I WILL CALL UPON THE LORD
Songs Of Prayer And Praise
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship