Loading Songs...

Ufuna Kuomoledwa Kodi

[1]
Ufuna kuomboledwa kodi? Iripo mphamvu mwazi wace;
Ufuna kugonjetsa zoipa? Muli mphamvu m’mwazi wace.

Chorus:
Muli mphamvu (m’mwazi) yozwizwitsatu, M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu, Mmwazi wa mwana wa nkhosa

[2]
Ufuna kuleka kunyada? Iripo mphamvu m’mwazi wace;
Idzatu pa mtanda nutsukidwe, Muli mphamvu m’mwazi wace.

[3]
Ufuna kuyera kopambana? Iripo mphamvu m’mwazi wace;
Zoipa zonse adzayeretsa, Muli mphamvu m’mwazi wace.

[4]
Ufuna kugwira ntchito yace? Iripo mphamvu m’mwazi wace;
Ufuna kumuyimbira Iye? Muli mphamvu m’mwazi wace.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

2 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Aliyeniokoa Aliyeniokoa
Kiswahili Praise And Worship
When The Roll Is Called Up Yonder When The Roll Is Called Up Yonder
Christ In Song Hymnal
Ancient Words Ancient Words
Golden Bells
Come Unto Me Come Unto Me
Christ In Song Hymnal
JOY TO THE WORLD JOY TO THE WORLD
Songs Of Prayer And Praise