Loading Songs...

Tiribe Mzinda M’dzikoli

[1]
Tiribe mzinda m’dzikoli wolimba, wokhalitsanso
Komatu tikondwera ’fe, Tifuna mnzinda udzawo,
Tifuna mzinda udzawo.

[2]
Tiribe mzinda m’dzikoli, Wolimba, wokhalitsanso;
Tifuna wina mmwambamo, Wowala ndi wosathanso
Wowala ndi wosathanso.

[3]
Ee, malo a mtenderewo, Otopawo apumako!
Ndikhala ndi mapikawo, Ndikadaulukirako,
Ndikadaulukirako.

[4]
Tonthola moyo wanga ’we, Adziwa nthawi Mlunguyo;
Ndicite ntchito yaceyo, Apatsa ’ne mpumulowo,
Apatsa ’ne mpumulowo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

4 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Jesus My Savior Jesus My Savior
Songs On Request
What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal
DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE?
Hymns Of Comfort
Glory Glory
Songs On Request