Loading Songs...

Tidzaima Bwanji Pa Ciweruzo

[1]
Mme ne Yesu adzasonkhatu, Mitundu yonse ya dziko,
Kodi tidzaima bwanji’fe Pa mpando waciweruzo?

CHORUS:
Adzasonkhanitsa tiriguyo, Koma mankhusu adzataya;
Nanga tidzaima bwanji ko’ Pa tsiku la ciweruzo?

[2]
Kodi tidzamva mau ace, Wacita bwino Iwetu,
Kapaena tidzanjenjemera, Tidzacotsedwa ku mpando?

[3]
Iye adzakondwera ndithu, Kuona oomboledwa,
Adzawabvekatu zobvala, Pa kugwadira Mbuyeyo.

[4]
T’yeni tidikire tsono, Ndi nyali zathu zowala,
Poitana Mkwati ku phwando Tidzakhale okonzeka.

[5]
Tikakhala okonzekatu, Tikakhala opirira;
Podatha ulendo wathuwu, Tidzanka naye kumwamba.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
Wade In The Water Wade In The Water
Songs On Request
How Great Thou Art How Great Thou Art
Spiritual Songs
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise
Here I Am To Worship Here I Am To Worship
Hillsong United