Loading Songs...

Thandwe Lolimba

[1]
Sindikhulupira win Koma dzina la Yesuyo.

CHORUS
Ndaima pa Krisu Thandwe, Nthaka yonse ndi mcenga,
Nthaka yonse ndiyo mcenga.

[2]
Pondiphimba ine mdima, Ndipumula mwa Iyeyo,
M’namondwe ndi m’nphepo zonse, Ndithawira kwa Iyeyo.

[3]
Pangano lake ndi mwazi, Zindichinjiriza ine,
Ndikalepheratu pena, Ndidzakhalatu mwa Iye.

[4]
Pamene Iye adzadza, Ndidzapezeke mwa Iye,
Ndiri m’cilungamo cace, Wopanda naye cifukwa.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
Kaa Nami Kaa Nami
Kiswahili Praise And Worship
I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise
Ancient Words Ancient Words
Songs On Request
Ancient Words Ancient Words
Golden Bells
Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship