Tamva Mau Omwewo
[1]
Tamva mau omwewo, Atitu Yesuyo;
Mpulumutsi ndiyedi, Yesuyo, Yesuyo;
Pita m’midzi monsemo, Dziko losne limvetu,
Pita iwe konseko, Mveratu Mbuyeyo.
[2]
Lalikani nanunso, Yesuyo, Yesuyo;
Kwa ocima onsewo, Amve za mbuyeyo.
Lalikirani m’zisimo, Ndi m’mapiri monsemo;
Kuti onse amvetu, Yesuyo, Yesuyo.
[3]
Yimbadi za Iyeyo, Amvetu anthuwo;
Kuti Yesu wafadi, Kalelo, kalelo.
Atikonda ifetu, Natifera indedi.
Kucotsera chimoli, Yesuyo, Yesuyo.
[4]
Bukitsani maunso, Konseko, Konseko.
Aitana anthuwo, Ponsepo, Ponsepo.
Kodi wina samvatu? Pitako, pitako ’we,
Angofuna onsewo, Yesuyo, Yesuyo.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.