Loading Songs...

Sitidziwa Nthawi Ya Kudza

[1]
Sitidziwa nthawi yakudza kwa Mbuye, Koma zooneka pa dziko zinena
Adzabwera msanga, tikondwa, komatu sitidziwa nthawi.

Chorus:
Adzatu! Tikonzeke tilinde! Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wace, Komatu sitidziwa nthawi.

[2]
Ku’nika kulipo kwa anthu a nzeru, Co’nadi ciripo mu mau a Mlungu,
Alembic anena momveka, komatu sitidziwa nthawi

[3]
Tilinde, tipempe ndi nyali zowala, Tigwirenso ntchito mpakatu abwera
Poona zozizwa komatu sitidziwa nthawi.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Blessed Assurance Blessed Assurance
Christ In Song Hymnal
I WILL CALL UPON THE LORD I WILL CALL UPON THE LORD
Songs Of Prayer And Praise
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise
Listen To Our Hearts Listen To Our Hearts
Songs On Request