Sitidzalekananso
[1]
Tikakhala ndo abwenzitu, M’dziko lathu lino,
Posacedwa timalekana Nao mwa cisoni.
CHORUS
Sitidzalekana m’mwamba, Sitidzalekana,
M’dziko lokometsetsalo, Sitidzalekana.
[2]
Timakhala ndi c’yembekezo, Pakufa anzathu,
Kuti pakutha dziko lino, Tidzakhala nao.
[3]
Sitidzalekananso ai, M’dziko lokomalo,
Nyimbo za cimwemwe, mtendere, ’Dzayimba kosatha.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.