Loading Songs...

Sindipemphera, Mbuyanga

[1]
Sindipemphera, Mbuyanga, Za mawazo;
Mndipulumutse m’chimolo Lero lokha;
Mau ndisalankhulenso Oipawo;
Msungetu mlomo wangawu, Lero lino.

[2]
Ndzagwira ntchito yanuyo, Ndzapemphanso;
Ndikhalal wacifundoyo, Lero lokha;
Mundithandize, Mbuyanga, Kumera ’Nu;
Kuti ndidzipereketu pa leroli.

[3]
Ngatitu moyo wangawo Utha ndithu;
M’malonjezano anuwo ndikhalebe;
Sindipemphera, Mbuyanga, Za mawazo;
M’ndisunge m’manja mwanumo pa leroli.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Joy To The World Joy To The World
Christ In Song Hymnal
Aliyeniokoa Aliyeniokoa
Kiswahili Praise And Worship
I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise
What A Friend What A Friend
Golden Bells
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise