Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Sindidzakusiya

[1]
Sindidzakusiya konse, Sindidzakukananso;
Ndzatsogola ndzakusunga, Mongwa mwa dzina langa;
Musaope coipaco, pomvera malangizo.

[2]
Mphepo zikaomba mkuntho, upemphere kwa Ine;
Ndidzakufungata iwe, Kukusamala bwino;
Poyesedwa konyazitsa, Ndidzakuyendetsa bwino.

[3]
Mlengalenga pong’azima pakakoma ponsepo,
Madyerero osasowa, Zokondweretsa zokha;
Ndidzakhala nawe ndithu, Ndi kuti usacimwe.

[4]
Ngati ndadodometsedwa, Ndi nkhawa ndi cisoni,
Ngakhaletu kuli nkhungu, Ndidzakuunikira,
Mbendera yokwezekayi, Ya cikondi canga njo.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal