Loading Songs...

Sabata Nla Kupuma

[1]
Sabata nla kupuma, Ndi la cimwemweco,
Ndi tsiku lotonthoza, Lokometsetsatu;
Akuru ndi ang’ono, Tigwade tonsefe,
Tiyimbe kwa Woyera Wa nthawi zonsezo.

[2]
Sabata liri ngati Cocinjiriza ’fe,
Ndi monga ngati munda wotupa mdambomo;
Litsitsimutsa m’yoyo Ya akutopawo,
Popuma pa sabata Tiona mwambamo.

[3]
Ndi tsiku lakusinkha, Ndi la cikondico,
Lakuyanjana nazo Za mwambamwambamo;
Tipeze zakukoma Zoposa zinazo,
Tifuna kupumula kosatha mwambamo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Hillsong United
LORD OF ALL HOPEFULNESS LORD OF ALL HOPEFULNESS
Hymns Of Comfort
I Sing The Mighty Power I Sing The Mighty Power
Christ In Song Hymnal
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship