Loading Songs...

Poyambapo Ndakondwadi

[1]
Poyambapo ndakondwadi, Ntapeza Inu Mbuyetu,
Ndiyimba nyimbo yomweyi, Kukondwa sindikhala du.

CHORUS:
Kalelo! Kalelo! Wandisambitsa mmtimamo;
Wandiweruza lomwelo, Kupemba ndi kukondwako.
Kalelo! Kalelo! Wandisambitsa mmtimamo.

[2]
Ndamuza ndimakhalatu Ku nyumba kwace komweko;
Mnyamata wace ndinetu, Ndampatsa Mtima wonswewo.

[3]
Omwewo mapanganowo, Sitilekana ifetu.
Ndamvera ine mauwo, Wandiloleza m’mtimamo.

[4]
Ndampatsa Mtima wonsewo, Kupuma mwa Ambuyeyo:
Ndikhala, osamlekai, Kuthawa ndi kumsiya ’Ye.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE?
Hymns Of Comfort
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise