Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Pakwitana Mbuye Wanga

[1]
Pakwitana Mbuye wanga potsiriza dzikoli,
Pakufika tsiku la kuwalalo
Posonkhana akumvera, pakuona Yesuyo,
Ndidzakondwerera naye komweko

CHORUS:
Pakwitana Mbuye wanga (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wanga (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wanga,
Ndidzakondwerera naye komweko.

[2]
Poturuka mmanda mwao, anthu ace onsewo,
Tidzasanganatu nao nthawiyo.
Pauuka osankhidwa, nkuka naye Yesuyo,
Ndidzakondwerera naye komweko.

[3]
Tisaleke kugwirabe ntchito ya Mulunguyo,
Tibukitse mbiri yace mdzikoli,
Ndi podzatha moyo wathu ndi zintchito zathuzo,
Tidzakondwerera naye komweko.

CHORUS: (lotsiriza)
Pakwitana Mbuye wathu (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wathu (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wathu,Ndidzakondwerera naye komweko.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

A wonderful Saviour A wonderful Saviour Spiritual Songs
WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS Songs Of Prayer And Praise
Glory Glory Songs On Request
DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE? Hymns Of Comfort
Jesus My Savior Jesus My Savior Songs On Request
Kutembea Nawe Kutembea Nawe Kiswahili Praise And Worship