Loading Songs...

Pakakhala Cikondi

[1]
Pakakhala cikondi, Banja likondwa; Pakakhala cimwemwe, banja likondwa
Mtendere ukhalitsa, Masiku awo onse; akhala mu mtendere, Akakondana.

Chorus:
Chikondi mbanjamo; Akhala mu mtendere, akakondana.

2. M’nyumba muli cimwemwe, Akakondana; Mulibenso madano, Akakondana
Ana onse akondwa, Namveranso makolo; Moyo wao ukondwa, Akakondana.

[3]
Mulungu akondwera, akakondana; Dziko lonse likoma, Akakondana
Zonse zowazingazo, Zimawakondweretsa; Mulungu akondwera, akakondana.

[4]
Yesu mndilandire ’ne, Ndidzakondadi; Munandifera ine, Ndidzakondadi
Ndidzapumla ndithu, Wopanda nkhawa konse; Mwa cifundo canuco, Ndidzakondwadi.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

4 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kaa Nami Kaa Nami
Kiswahili Praise And Worship
Come We That Love The Lord Come We That Love The Lord
Christ In Song Hymnal
A Wonderful Savior A Wonderful Savior
Christ In Song Hymnal
Servant’s Song Servant’s Song
Songs On Request
Hide Me, Rock Of Ages Hide Me, Rock Of Ages
Songs On Request