Loading Songs...

Okunkhawo Ali Kuti

[1]
Okunkhawo alitu kutiko? Amene akunkhatu zabwino?
Kucoka mu dziko loipali, Pocita ndi mau a Mlunguyo?

Chorus:
Ndanitu adze kudzakunkha, Kusonkhanitsira anthu m’mwambamo?
Ndi yani atithandizeko, Pofunafuna zobalazo?

[2]
Pitani mu mphambano monsemo, Funani mupezemo abwino;
Pitani kwa anthu ponse ponse, Musonkhanitsire kumwambako.

[3]
Zobala zakhwima ponse ponse za m’dzikomu zilindira ife.
Okuntha acepa ku ntchitoyi, Zambiri zidzaonongekatu.

[4]
Anthuni idzani ndi zidazo, Kudzasonankhanitsa za m’mundamo;
Gwiranibe mpaka Ambuyeyo Adzabwera ali kukondwatu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
Immortally Arrayed Immortally Arrayed
Songs On Request
I LOVE YOU LORD I LOVE YOU LORD
Songs Of Prayer And Praise
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs
Come We That Love The Lord Come We That Love The Lord
Christ In Song Hymnal