Nyali Yanu Iwalire
[1]
Tate wathu wa Kumwamba, ’Natipatsa nyali’Ce,
Koma atiuza ife, Tiwalitse enawo.
Chorus:
Nyali yanu iwalire, Kusonyeza njirayo
Kwa ocimwa ndi ofo’ka, Njira yonka m’Mwambamo.
[2]
Kuli mdima m’dziko lino, Ndi namondwe wa bvuto,
Obvutika alindira Nyali yotsogozayo.
[3]
Konza nyali yako msanga, Pena wobvutikayo
Atayidwa mu mdima, Akapanda nyaliyo.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.