Loading Songs...

Nthawi Ya Pemphero

[1]
Nthawi ya pempheroyo, powerama ife,
Tisonkhana kwa Yesu, Ambuyathuyo;
Tikakhulupiratu adzatibisanso,
Tidzapeza mpumulo tikapempheratu.

Chorus:
Ndi yokomadi, nthawi ya pempho,
Tidzapeza mpumulo tikapempheratu

[2]
Nthawi ya pempheroyo, Yesu ali mfupi
Ndi cifundo caceco atimvera ’fe.
Atiuza nkhawazo, tizataye kwa ’Ye,
Tidzapeza mpumulo, tikapempheratu.

[3]
Nthawi ya pempheroyo, akuyesedwawo
Amatula kwa Yesu zisoni zawo;
Yesu wacifundoyo amazicotsatu,
Tidzapeza mpumulo tikapempheratu.

[4]
Nthawi ya pempheroyo tikhulupiranso
Kuti zomwe tisowa tilandiradi;
Tikakhulupiradi nkhawa zicokanso;
Tidzapeza mpumulo tikapempheratu



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
JOY TO THE WORLD JOY TO THE WORLD
Songs Of Prayer And Praise
Sing The Wondrous Love Sing The Wondrous Love
Spiritual Songs
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship