Loading Songs...

Nthano Ya Yesu Uzeni

[1]
Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu;
Nthano yodala uzeni, Nthano yoposa zonse.
Nyimbo ya ’ngelo uzeni, Nthawi yobadwa Yesu,
Ulemelero kwa Mlungu, Ndipo mtendere pano.

CHORUS:
Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu,
Ntahno yodala uzeni, Nthano yoposa zonse.

[2]
Nena masiku ajawo, Mbuye nasala kudya,
Anayesedwa koopsya, koma analakika
Za ntchito yace uzeni, Ndi za zisoni zace,
Anazunzidwa kolimba, Mphawi wopanda kwao.

[3]
Za mtanda wace uzeni, Ndi za zowawa zace,
Za manda ace uzeni, Ndi za kuuka kwace.
M’nthano ndiona cikondi, Ca Yesu, Mbuye wanga,
Mmene ndiimva ndilira, Anaombola ine.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

2 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Umetamalaki Umetamalaki
Songs On Request
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
God Bless You, Go With God God Bless You, Go With God
Songs On Request
Come We That Love The Lord Come We That Love The Lord
Christ In Song Hymnal
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise