Ntayenda Nanu
[1]
Ntayenda nanu Mulungu!
Ngati a Kumwamba,
Ntaunikidwa panjira,
Yofitsa kwa Yesu.
[2]
Mzimu Woyera bwerani,
Mtehnga wa mpumulo;
Ndidana nazo zoipa,
Zotilekanitsa.
[3]
Ndinakondwa nthawi ija!
Sindingaiwaile,
Ndatsala m’zobvuta zokha,
Dziko ndi lacabe.
[4]
Fano ndinalikondalo,
Kaya ndi lotani,
Thangateni kulicotsa,
nditsale ndi Inu.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.