Loading Songs...

Ndiyimba Mu Mtima Mokondwa

[1]
Ndiyimba mu Mtima mokondwa! Ndi nyimbo yokoma, yoyera;
Ndiyimba za Yesu Mbuyanga, Anditonthozane phe!

Chorus:
Cete! Cete! M’mtima mtenderemu phe;
Udzera kwa Yesu wokonda, Mtendere mu mtimamu.

[2]
Pa mtanda Mbuyanga nafera, Adandicotsera zocimwa;
Anandigulira mtendere, Anditonthozane phe!

[3]
Pomsankha Yesuyo Mbuyanga, Mtendere walowa mu Mtima;
Ndapeza dalitso loposa, Anditonthozane phe!

[4]
Pokonda Yesuyo, mtendere, Ku nthawi zosatha mtendere;
Potsata Mbuyanga apatsa, Mtendere mu mtimamu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Hillsong United
Here I Am To Worship Here I Am To Worship
Hillsong United
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
Ancient Words Ancient Words
Songs On Request
He Gave Me A Song He Gave Me A Song
Songs On Request
I WILL SING OF THE MERCIES I WILL SING OF THE MERCIES
Hymns Of Comfort