Loading Songs...

Ndiyeretu Mbu

[1]
Ambuye ndifuna nditsukenitu, Mukhalitse ndine mu mtima’ngamu;
Mutyole zonsezo zodetsa’netu, Musambitse ine, ndiyeretu mbu!

CHORUS
Ndiyeretu mbu, E, ndiyeretu mbu,
Musambitse ine, ndiyeretu mbu.

[2]
Ambuye taonani pansi pano, Kuti m’ndithandize kudzipereka;
Ndileke zangazo zoipsa’netu, Musambitse ine, Ndiyeretu mbu.

[3]
Cifukwa ca ici ndipepheratu, Ndidikira Inu Ambuyanga ’Nu;
Ndikhulupilira pa mwaziwo pyu, Musambitse ine Ndiyeretu mbu.

[4]
Ambuye muona ndidikira’Nu, Idzani kukonzetsa mtima wanga;
omwe akufuna simuwakana, Musambitse ine, ndiyeretu mbu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Christ In Song Hymnal
Blessed Assurance Blessed Assurance
Christ In Song Hymnal
Amazing Grace Amazing Grace
Golden Bells