Loading Songs...

Ndisauka Ndinacimwa

[1]
Ndisauka ndinacimwa, Koma Inu mwandifera,
Ndipo ndamva mundi’tana, Mwana Mlungu ndingobwera.

[2]
Ndisauka ndimasowa, Mphamvu ya kuyera mtima,
Mwazi wanu unditsuka; Mwana Mlungu ndingobwera.

[3]
Ndisauka, sindikhoza Kwiletsa nkhondo mu mtima,
Ndi cisoni, mantha, nkhawa, Mwana Mlungu ndingobwera.

[4]
Ndisauka sindiona, Ndimadwala ndilefuka,
Zonse ndizitaya kwa ’Nu, Mwana Mlungu ndingobwera.

[5]
Inde, Yesu mulandira, Muciritsa mpulumutsa,
Mau anu ndibvomera, Mwana Mlungu ndingobwera.

[6]
Inde, Yesu, mundikonda, Zonse zina ndazitaya,
Tsono kukakhala wanu, Mwana Mlungu ndingobwera.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Victory In Jesus Victory In Jesus
Golden Bells
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Christ In Song Hymnal
10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
HOW GREAT THOU ART HOW GREAT THOU ART
Songs Of Prayer And Praise
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise