Loading Songs...

Ndingayere Bwanji ’Ne

[1]
Ndingayere bwanji ’ne? Mwazi wa Ambuye Yesu.
Nc’ani cindicizanso? Mwazi wa Ambuye Yesu.

CHORUS:
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo

[2]
Pakudetswa ndiona, Mwazi wa Ambuye yesu
Pakucimwa ndichula, Mwazi wa Ambuye Yesu

[3]
Zina sizikwanatu, Mwazi wa Ambuye ndiwo.
Ntchito zanga zicepa, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[4]
Ndimakhulupiradi, Mwazi wa Ambuye Yesu
Zolungama zangazi, Mwazi wa Ambuye Yesu

[5]
Poyamika ndiyimba Mwazi wa Ambuye Yesu.
Ndithokoza Mbuyanga, Mwazi wa Ambuye Yesu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Glory Glory
Songs On Request
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal
I WILL SING OF THE MERCIES I WILL SING OF THE MERCIES
Hymns Of Comfort
Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs