Loading Songs...

Ndine Wanuyo

[1]
Ndine wanuyo, ndamva mauwo, A cikondi canuco;
Mundikoketu mfupi ndinuyo, Mwa cikhulupiroco.

Chorus:
Mndisendeze (mfupi), mfupi mbuyanga, Ndi pa mtanda wanuwo;
Mndisendeze mfupi, Mbuye wanga ’Nu, Ndi pa mwazi wanuwo.

[2]
M’nchito yanu mndipatulire ’ne, Mwa cisomo canuco;
Moyo wangawo uyang’ane ’Nu, Ndicitetu zanuzo.

[3]
Ndikondwera ’ne pakupitatu, Kugwadira Mbuyeyo;
Pakunenenatu naye mtserimo, Monga bwenzi langalo.

[4]
Sindidziwatu za cikondico, Mpaka n’dzanke tsidyalo;
Sindifikira za cimwemweco, Mpaka n’dzanke kwanuko.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
Listen To Our Hearts Listen To Our Hearts
Songs On Request
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
A wonderful Saviour A wonderful Saviour
Spiritual Songs