Loading Songs...

Ndine Njira

[1]
Monga nkhosa zotayika, Zomwazika konse;
Zasiya moyo, mtendere, Njira yandisowa?

Chorus:
Sap, & alto:
Ndine njira, co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa Ine,
Ndine njira, co’nadi, moyo,
Sungafike Atate komwa mwa Ine

Bass & Ten:
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moo
Sungafike Atate koma mwa ine
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa ine

[2]
Nkhawa zandisokoneza, Mulungu ndifuna;
Manena-nena ngambiri, Ndingagwire ziti?

[3]
Kwa Kristu, njira, co’nadi Ndi moyo ndibweranso;
Adzandifitsa kwa Tate, Kumalo kosatha.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Glory Glory
Songs On Request
I WILL SING OF THE MERCIES I WILL SING OF THE MERCIES
Hymns Of Comfort
Abide With Me Abide With Me
Golden Bells
What A Friend What A Friend
Golden Bells
I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise