Loading Songs...

Ndikweze Yesu Yekha

[1]
Ndikweze yesu yekha m’zinthu zonse;
Amveke, aoneke yekhayo;
Mu ntchito, m’maganizo ndipo m’mau
Ambuye aoneke yekhayo.

[2]
Ndi Yesu atonthoza akulira
Yekhayo angacotse msoziwo;
Yekhayo angatule akatundu
Yekhayo angacotse manthawo.

[3]
Ndileke mau onse ena cabe,
Ndileke zakupusa zangazi
Ndikweze Yesu ndisanyade konse,
Ndisadzitame koma Iyeyo.

[4]
Ndi Kristu amapatsa ’ne zosowa
Ndi yekha amapatas mphamvunso
Yekhayo m’thupi , m’moyo, ndi mu mzimu
Ndi Kristu yekha nthawi zonsezo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

2 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

He Gave Me A Song He Gave Me A Song
Songs On Request
Joy to the World Joy to the World
Sunday School Songs
See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request
Umetamalaki Umetamalaki
Songs On Request
Ancient Words Ancient Words
Songs On Request