Loading Songs...

Ndikonda, Ndikonda Ambuyanga

[1]
Ndikonda, ndikonda Ambuyanga ’Nu;
Ndiknda Yesuyo, Mpulumutsitu.
Ndikonda inuyo mudziwadi;
Zintchito zinena kukonga kwanga.

[2]
Ndikndwa, ndikondwa kopambanadi!
Ndaima pa phiri ndiyang’anitsa
Ku mzinda woyera ndkakhaleko,
Ndi Yesu, angeo, ndi anzangawo.

[3]
Yesu ’Nu, Mp’lumutsi, mndidalitsetu,
Ndinutu cimwemwe mpumulo wanga.
Ndiyimba cikondi ca Mbuyangayo;
Cisomo canuco cindidzaza ’ne.

[4]
Ndaniyo oposa Mpulumutsiyo?
Akonda inenso nan’thangata ’ne.
Ndiyamika Mbuye, ndiyimbira ’Ye,
Ndikndwa koposa mu mtimangamo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request
ABIDE WITH ME ABIDE WITH ME
Hymns Of Comfort
I LOVE YOU LORD I LOVE YOU LORD
Songs Of Prayer And Praise
Servant’s Song Servant’s Song
Songs On Request
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort