Loading Songs...

Ndiganiza Za Dziko Lokometsa

[1]
Ndiganiza za dziko lokometsalo, Komwe nzafikako tsikulo;
Podzaima pa mbali M’lumutsiyo, Ndidzavala nyenyezizo ko?

CHORUS:
Ndidzabvala nyenyezizo ko, Mbuyanga, Mmene dzuwa lidzalowadi (lowadi)
Mmene ndazuka mmalo a mpumulo, Ndidzabvala nyenyezizo ko (tsikulo)

[2]
M’mphamvu yaceyo ndigwiretu ntchitoyo, Kuti ndikopetu anthuwo;
Kuti ndzapate nyenyezi pa tsikulo, Mmene Mbuye ’dzayamika ’fe.

[3]
Ndidzakondwera poona Mbuyanga, Ndikupereka mituloyo;
Ndidzakondwera m’mzinda wa golidiwo, Ndikadzabvala nyenyezizo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

I Sing The Mighty Power I Sing The Mighty Power
Christ In Song Hymnal
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort
Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship