Loading Songs...

Ndifuna Inu, Mbuyanga

[1]
Ndifuna Inu, Mbuyanga, Cifukwa ndagwa mthopemo,
Ndi madzi pena motowo, Mnditsuke ’ne, mnditsuke ’ne.

CHORUS:
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Acoketu mu mtimanga.

[2]
Mukatsegula masowa, Ndidzakuyamikani ’Nu.
Komabe Mtima woyera Udzapambana zonsezo.

[3]
Ukutsukidwa mtimawo Adzatseguka masowo.
Cifukwa kuti mwa Inu, Ndionamo za mmwambamo.

[4]
Ndayesa kudzikonzatu, Kucotsa chimo langalo
Ngakhale ndayesetsatu, Zoipazo ziripobe.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Joy To The World Joy To The World
Caroling Songs
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
Ill Fly Away Ill Fly Away
Golden Bells
A wonderful Saviour A wonderful Saviour
Spiritual Songs
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request