Loading Songs...

Ndidziwitsitsa Yesu Ngwanga

[1]
Ndidziwaitsitsa yesu ngwanga; Tsiku ndi tsiku ndimakondwera.
Anandigula ndi mwazi ’ce, Anandipatsa Mzimu wace.

Chorus:
Mau omwewo, Nyimbo yomwe, Yesu ndimtama tsiku lonse
Mau omwewo, Nyimbo yomwe, Yesu ndimtama tsiku lonse

[2]
Nkamvera Yesu ndikondwatu, Ndiyang’anitsa Ambuyangayo
Ndipo angelo atengera Ine cisomo ndi cumanso

[3]
Ndine kapolo Mbuyanga, Andigwiritsa zintchito zace
Ndimyembekeza ’dzabweranso, Adzanditenga kwawo mmwamba.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
What A Friend What A Friend
Golden Bells
I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise
God Bless You, Go With God God Bless You, Go With God
Songs On Request
See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request
Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells