Loading Songs...

Ndidze Pafupi Ndi Inu

[1]
Ndidze pafupi ndi Inutu, Yesu, Mombolo wopambana ’Nu;
Inu mndisunge mmnaja mwanu, Inu mndibise pa ngaka yanu,
Inu mndibise pa ngaka yanu.

[2]
Ndidza pafupi ndekha, Kanthu ndiribe kopatsa Yesu;
Mtima woipa ndipatsa ’Nu, Munditsuketu ndi mwazi wanu,
Munditsuketu ndi mwazi wanu.

[3]
Ndidza pafupi, ndine wanu, Ine ndisiya zoipa zonse;
Zonse zonyada za dzikoli, Koma mndipatse Ambuye Yesu,
Koma mndipatse Ambuye.

[4]
Ndidza pafupi ndinu, Mbuye, Mpaka kumwamba ndidzalowatu,
Nthawi zosatha n’dzakhalabe, Pafupifupi ndi Mp’lumutsiyo,
Pafupifupi ndi Mp’lumutsiyo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

GIVE THANKS GIVE THANKS
Songs Of Prayer And Praise
He Gave Me A Song He Gave Me A Song
Songs On Request
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
I LOVE YOU LORD I LOVE YOU LORD
Songs Of Prayer And Praise
Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Christ In Song Hymnal
What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal