Loading Songs...

Ndidzakutsatani

[1]
Ndidzakutsani Mbuye, Kuli konse mupita;
Ndzakutsani Mbuye, Inde n’dakutsatani.

CHORUS:
Ndidzakutsatani Mbuye, Yemwe munandifera;
Ngakhale akukaneni, Ndidzakutsatani ’Nu.

[2]
Nkana njira ndi yaminga Yopanda matakazo,
Mukandikonzera Ine, Mokondwa n’dzatsata ’nu.

[3]
Nkana cisautso cidza, Kapena ndiyesedwa;
Mbuyenso anayesendwa, ndidzamsata mokondwa.

[4]
Nkana ndipeze mabvuto, Sindizakukanani;
Mnazunzidwanso koopsa Ndidzatsatabe Inu.

[5]
M’mafunde ndi mozamammo, Mudzanditsogolera;
M’nayenda m’mafunde kale, Ndidzakutsatani ’Nu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal
Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship
When The Roll Is Called Up Yonder When The Roll Is Called Up Yonder
Christ In Song Hymnal
Blessed Assurance Blessed Assurance
Spiritual Songs
10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request