Loading Songs...

N’kwabwino Kukhulupirira

[1]
N’kabwino kukhulupira, M’mau ace a yesu;
Kupuma m’malonjezo’ce, Ndimtama nthawi zonse.

CHORUS:
Ndikhulupirira Yesu, Ndimtama nthawi zonse;
Yesu ali wa chifundo, Ndimtama nthawi zonse.

[2]
N’kwabwino kukhulupira, Mwazi wace wa Yesu;
Kungomkhulupira Iye Adzatitsuka ife.

[3]
N’kwabwino kukhulupira, Kuti acotse cimo;
Nadzatipatsa’fe moyo, Cimwemwe ndi mtendero.

[4]
Ndikondwa kumdziwa Iye, Mpulumutsi wangayo;
N’dziwa adzakhala nane, Mpaka cimariziro.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship
Listen To Our Hearts Listen To Our Hearts
Songs On Request
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
Amazing Grace Amazing Grace
Golden Bells