Loading Songs...

Muyamikeni Yesu

[1]
Nyamikeni! Yesu wodala Mombolo!
Yimba cikondi cozizwitsadi!
Mkondwereni mkuru wa angelo m’Mwamba,
Dzina lace lilimekezedwe!
Monga mbusa asunga ana,
M’mikono mwace awanyamula.

Chorus:
Myamikeni! Ali wamkuru koposa;
Myamikeni m’nyimbo zokondwera.

[2]
Myamikeni! Yesu wodala Mombolo!
Zathu zocimwa nathira mwazi;
Ndiye Thanthwe lathu la cipulumutso,
Myamikeni Yesu wopacikikwa;
Mbukitseni! Yesu wotithangata,
Cikondi cosamariza ncace.

[3]
Myamikeni! Yesu wodala mombolo!
Khomo m’mwamba mumveka hosanna!
Yesu Mbuye alera nthawi zosatha;
Mbveke krona Wansembe ndi mfumu!
Kristu adza wogonjetsa dzikoli,
Mphavu ndi ulemu ndi za Yesu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Amazing Grace Amazing Grace
Golden Bells
Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise
DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE?
Hymns Of Comfort
Ill Fly Away Ill Fly Away
Golden Bells