Mumbveke Mbuyeyo
[1]
Tamani mphamvu ya Yesu angelo agwade;
Turutsanitu korona mumbveke, Mbuyeyo
Turutssanitu korona mumbveko Mbuyeyo.
[2]
Inu osankhidwa ace, Oomboledwa’nu
Tamani Mpulumutsiyo, mubweke Mbuyeyo;
Tamani Mpulumutsiyo mumbveko Mbuyeyo.
[3]
Anthu onse ndi mitundu, Pa dziko linotu,
Am’lemekezu Mfumuyo, mumbveke Mbuyeyo;
Am’lemekeze Mfumuyo, mumbveke Mbuyeyo.
[4]
Tifuna kuti komweko, Tikamgwadire’Ye
Tidzayimba kosaleka mumbveke Mbuyeyo
Tidzayimba kosaleka mumbveke Mbuyeyo.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.