Loading Songs...

Mulungu Atsogoza ’Ne

[1]
Mulungu atsogoza ’Ne, Ndapuma m’mtima mwangamo.
Ayang’anira m’njiramo, Poyenda ine konseko.

CHORUS:
Mulungu atsogoza ’ne, Ndi dzanja-dzanja lacelo.
Ndidzamtsatira Mbuyanga, Poyenda ine konseko.

[2]
Masiku ena mdima bi, Ndimabvutika m’mtimamo.
Pa nthawi zina nkondwadi, Popeza zokondwetsazo.

[3]
Ndzagwira dzanja lanulo, Osang’ung’udza konsei.
Ndidzaka mokondweratu, pomtsata Mbuye wangayo.

[4]
Podzatha ntchito yangayi, Podzagonjetsa chimolo.
Kumene ndidzakhalatu, Sindidzaopa imfayo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Come We That Love The Lord Come We That Love The Lord
Christ In Song Hymnal
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort
10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
Glory Glory
Songs On Request
How Great Thou Art How Great Thou Art
Spiritual Songs