Loading Songs...

Mulungu Akhala Ndi Inu

[1]
Mulungu akhale ndi inu, Mpaka tidzaonananso;
Atsogoze, asunge ’nu; Mulungu akhale ndi inu.

CHORUS:
Asunga nonsenu, Tikomana ndi Yesu,
Asunga nonsenu, Mulungu akhale ndi inu.

[2]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi mapiko akubisa,
Masiku onse kudyetsa; Mulungu akhale ndi inu.

[3]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi pamene mubvutika,
Adzakuthangatani ’nu, Mulungu akhale ndi inu.

[4]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi cikondi cace conse,
Asunge mzoopsya zonse, Mulungu akhale ndi inu.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Glory Glory
Songs On Request
Ancient Words Ancient Words
Golden Bells
Umetamalaki Umetamalaki
Songs On Request
HOW GREAT THOU ART HOW GREAT THOU ART
Songs Of Prayer And Praise
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise
See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request