Loading Songs...

Mulungu, Mfumu

[1]
Mulungu, Mfumu ’Nu, Ndiribe mphamvutu,
Munandilenga, mundisunga Nthawi zonsezi
Munandilenga, Mundisunga Nthawi zonsezi.

[2]
Ndiribe winanso, Ndimatsamira ’Nu;
Zabwino zanu zipambana, Ndicitenji ko?
Zabwino zanu zipambana, Ndicitenji ko?

[3]
Ndipatse ciani ko? Poona zonsezi
Zakhala zanu kale ndithu, Ndidzatani ko?
Zakhala zanukale ndithu. Ndidzatani ko?

[4]
Mufuna mtimangu, Ndipatsa msangatu.
Ndikhale wanu nthawi zonse, Mndilandire ’ne.
Ndikhale wanu nthawi zonse, Mndilandire ’ne.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Abide With Me Abide With Me
Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance
Golden Bells
10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Hymns Of Comfort
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort