Loading Songs...

Muli Dzuwa M’phiri Muja

[1]
Muli dzuwa m’phiri muja, Muli dzuwa m’nyanjamo;
K’wala kwace kumagwera Pa maudzu ponsepo;
Koma dzuwa lopambana Liri m’tima mwangamu;
Ka’mba komwe mukhalitsa, Kuli dzuwa lowala.

Chorus:
Muli dzuwa lakuwalitsa! Muli dzulwa m’timanga.
Yesu adzacotsa mdima, Muli dzuwa m’timanga.

[2]
Ndisiya ’ne nsoni zanga Ndi zobvala za nsanza;
Mundibvekatu zoyera, Ndiyamika m’mtimamo’
Kuli malo a ulemu Munandikonzera ’ne;
Mtima wanga ufunako, Ndizatsa Inutu.

[3]
Inu, Yesu, Mwandigula, Ndine wanu konseko,
Munayatsa nyali yanga, Iwalire Inuyo;
Kuli malo a ulemu Munandikonzera ’ne,
Mtima wanga ufunako, Ndidzatsa Inuyo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

5 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Immortally Arrayed Immortally Arrayed
Songs On Request
Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Hillsong United
Does Jesus Care Does Jesus Care
Golden Bells
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs
A Wonderful Savior A Wonderful Savior
Christ In Song Hymnal
Wade In The Water Wade In The Water
Songs On Request